Yesaya 41:19 BL92

19 Ndidzabzala m'cipululu mkungudza, ndi msangu, ndi mcisu, ndi mtengo waazitona; ndidzaika m'cipululu pamodzi mlombwa, ndi mkuyu, ndi naphini;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 41

Onani Yesaya 41:19 nkhani