Yesaya 41:20 BL92

20 kuti iwo aone ndi kudziwa, ndi kulingalira, ndi kumvetsa pamodzi, kuti dzanja la Yehova lacita ici, ndipo Woyera wa Israyeli wacilenga ici.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 41

Onani Yesaya 41:20 nkhani