Yesaya 43:25 BL92

25 Ine, Inedi, ndine amene ndifafaniza zolakwa zako, cifukwa ca Ine mwini; ndipo Ine sindidzakumbukira macimo ako.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 43

Onani Yesaya 43:25 nkhani