Yesaya 43:3 BL92

3 Cifukwa kuti Ine ndine Yehova Mulungu wako, Woyera wa Israyeli, Mpulumutsi wako; ndapatsa Aigupto dombolo lako, Etiopia ndi Seba m'malo mwako.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 43

Onani Yesaya 43:3 nkhani