Yesaya 43:4 BL92

4 Pokhala iwe wa mtengo wapatari pamaso panga, ndi wolemekezeka, ndipo ndakukonda iwe; Ine ndidzakuombola ndi anthu, ndi kupereka anthu m'malo mwa moyo wako.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 43

Onani Yesaya 43:4 nkhani