Yesaya 43:5 BL92

5 Usaope; pakuti Ine ndiri ndi iwe; ndidzatenga mbeu zako kucokera kum'mawa, ndi kusonkhanitsa iwe kucokera kumadzulo.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 43

Onani Yesaya 43:5 nkhani