Yesaya 5:19 BL92

19 amene ati, Mlekeni iye akangaze, mlekeni iye afulumize nchito yace kuti ife tione; ndipo lekani uphungu wa Woyera wa Israyeli uyandikire, udze kuti tiudziwe!

Werengani mutu wathunthu Yesaya 5

Onani Yesaya 5:19 nkhani