Yesaya 5:28 BL92

28 amene mibvi yao ili yakuthwa, ndi mauta ao onse athifuka; ziboda za akavalo ao zidzayesedwa ngati mwala, ndi njinga zao ngati kabvumvulu;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 5

Onani Yesaya 5:28 nkhani