Yesaya 5:29 BL92

29 kubangula kwao kudzafana ndi mkango, iwo adzabangula ngati ana a mikango, inde iwo adzabangula, nadzagwira nyama, naicotsa bwino opanda wakupulumutsa.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 5

Onani Yesaya 5:29 nkhani