Yesaya 5:30 BL92

30 Ndipo iwo adzawabangulira tsiku limenelo ngati kukokoma kwa nyanja; ndipo wina ayang'ana padziko, taonani mdima ndi nsautso, kuyera kwadetsedwanso m'mitambo yace.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 5

Onani Yesaya 5:30 nkhani