Yesaya 6:1 BL92

1 Caka cimene mfumu Uziya anafa, ndinaona Ambuye atakhala pa mpando wacifumu wautari, ndi wotukulidwa, ndi zobvala zace zinadzala m'Kacisi.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 6

Onani Yesaya 6:1 nkhani