7 Mverani Ine, inu amene mudziwa cilungamo, anthu amene mumtima mwao muli lamulo langa; musaope citonzo ca anthu, ngakhale kuopsedwa ndi kutukwana kwao.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 51
Onani Yesaya 51:7 nkhani