8 Pakuti njenjete idzawadya ngati copfunda, ndi mbozi zidzawadya ngati ubweya; koma cilungamo canga cidzakhala ku nthawi zonse, ndi cipulumutso canga ku mibadwo yonse.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 51
Onani Yesaya 51:8 nkhani