11 Cokani inu, cokani inu, turukani ku Babulo; musakhudze kanthu kodetsa; turukani pakati pace, khalani okonzeka, inu amene munyamula zotengera za Yehova.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 52
Onani Yesaya 52:11 nkhani