12 Pakuti simudzacoka mofulumira, kapena kunka mothawa; pakuti Yehova adzakutsogolerani, ndi Mulungu wa Israyeli adzadikira pambuyo panu.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 52
Onani Yesaya 52:12 nkhani