1 Pfuula zolimba, usalekerere, kweza mau ako ngati lipenga, ndi kuwafotokozera anthu anga colakwa cao, ndi banja la Yakobo macimo ao.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 58
Onani Yesaya 58:1 nkhani