Yesaya 58:10 BL92

10 ndipo ngati upereka kwa wanjala cimene moyo Iwako umakhumba, ndi kukhutitsa moyo wobvutidwa, pomwepo kuunika kwako kudzauka mumdima, ndipo usiku wako udzanga usana;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 58

Onani Yesaya 58:10 nkhani