9 Pamenepo udzaitana, ndipo Yehova adzayankha; udzapfuula ndipo Iye adzati, Ndine pano. Ngati ucotsa pakati pa iwe gori, kukodolana moipa, ndi kulankhula moipa,
Werengani mutu wathunthu Yesaya 58
Onani Yesaya 58:9 nkhani