11 Tonse tibangula ngati zirombo, ndi kulira maliro zolimba ngati nkhunda; tiyang'anira ciweruziro koma palibe; tiyang'anira cipulumutso koma ciri patari ndi ife.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 59
Onani Yesaya 59:11 nkhani