Yesaya 59:10 BL92

10 Tiyambasira khoma ngati wakhungu, inde tiyambasa monga iwo opanda maso; tipunthwa usana monga m'cizirezire; tiri m'malo amdima ngati akufa.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 59

Onani Yesaya 59:10 nkhani