Yesaya 59:9 BL92

9 Cifukwa cace ciweruziro ciri patari ndi ife, ndi cilungamo sicitipeza; tiyang'anira kuunika, koma taona mdima; tiyang'anira kuyera, koma tiyenda m'usiku.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 59

Onani Yesaya 59:9 nkhani