Yesaya 59:8 BL92

8 Njira ya mtendere saidziwa, ndipo palibe ciweruziro m'mayendedwe mwao; akhotetsa njira zao; ali yense ayenda m'menemo sadziwa mtendere.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 59

Onani Yesaya 59:8 nkhani