7 Mapazi ao athamangira koipa, ndipo iwo afulumira kukhetsa mwazi wosacimwa; maganizo ao ali maganizo oipa; bwinja ndi cipasuko ziri m'njira mwao.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 59
Onani Yesaya 59:7 nkhani