4 Palibe woturutsa mlandu molungama, ndipo palibe wonena zoona; iwo akhulupirira mwacabe, nanena zonama; iwo atenga kusayeruzika ndi kubala mphulupulu,
Werengani mutu wathunthu Yesaya 59
Onani Yesaya 59:4 nkhani