Yesaya 59:5 BL92

5 Iwo afungatira mazira a mamba aswetse, naluka ukonde wa tandaude; iye amene adya mazira ace amafa, ndi coswanyikaco cisweka nicikhala songo.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 59

Onani Yesaya 59:5 nkhani