Yesaya 61:8 BL92

8 Pakuti Ine Yehova ndikonda ciweruziro, ndida cifwamba ndi coipa; ndipo ndidzawapatsa mphotho yao m'zoonadi; ndipo ndidzapangana nao pangano losatha.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 61

Onani Yesaya 61:8 nkhani