9 Ndipo ana ao adzadziwidwa mwa amitundu, ndi obadwa ao mwa anthu; onse amene awaona adzawazindikira kuti iwo ndiwo ana amene Yehova wadalitsa.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 61
Onani Yesaya 61:9 nkhani