10 Pitani, pitani pazipata; konzani njira ya anthu; undani, undani khwalala; cotsani miyala, kwezani mbendera ya anthu.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 62
Onani Yesaya 62:10 nkhani