Yesaya 62:9 BL92

9 koma iwo amene adzakolola adzadya ndi kutamanda Yehova; ndi iwo amene adzamchera adzamumwa m'mabwalo a kacisi wanga.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 62

Onani Yesaya 62:9 nkhani