Yesaya 65:4 BL92

4 amene akhala pakati pa manda, ndi kugona m'malo am'tseri; amene adya nyama ya nkhumba, ndi msuzi wa zinthu zonyansa uli m'mbale zao;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 65

Onani Yesaya 65:4 nkhani