23 Ndipo kudzakhala kuti kuyambira pa mwezi wokhala kufikira ku unzace, ndi kuyambira pa Sabata lina kufikira ku linzace, anthu onse adzafika kudzapembedzera pamaso pa Ine, ati Yehova.
Werengani mutu wathunthu Yesaya 66
Onani Yesaya 66:23 nkhani