Yesaya 66:24 BL92

24 Ndipo iwo adzaturuka ndi kuyang'ana mitembo ya anthu amene andilakwira Ine, pakuti mbozi yao sidzafa, pena moto wao sudzazimidwa; ndipo iwo adzanyansa anthu onse.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 66

Onani Yesaya 66:24 nkhani