Yesaya 7:25 BL92

25 Ndipo zitunda zonse zinalimidwa ndi khasu, iwe sudzafikako cifukwa ca kuopa lunguzi ndi minga, koma pomwepo padzakhala potumizira ng'ombe ndi popondaponda nkhosa.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 7

Onani Yesaya 7:25 nkhani