Yesaya 8:1 BL92

1 Ndipo Yehova anati kwa ine, Tenga iwe polembapo papakuru, nulembe pamenepo ndi malembedwe odziwika, Kangazakufunkha Fulumirakusakaza,

Werengani mutu wathunthu Yesaya 8

Onani Yesaya 8:1 nkhani