14 Mwapenya; pakuti mumayang'anira cibvutitso ndi cisoni kuti acipereke m'manja mwanu;Waumphawi adzipereka kwa Inu;Wamasiye mumakhala mthandizi wace.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 10
Onani Masalmo 10:14 nkhani