1 Yehova, mtima wanga sunadzikuzaNdi maso anga sanakwezeka;Ndipo sindinatsata zazikuru,Kapena zodabwiza zondiposa.
2 Indedi, ndinalinganiza ndi kutontholetsa moyo wanga;Ngati mwana womletsa kuyamwa amace,Moyo wanga ndiri nao ngati mwana womletsa kuyamwa.
3 Israyeli, uyembekezere Yehova,Kuyambira tsopano kufikira kosatha.