2 Ndidzacita mwanzeru m'njira yangwiro;Mudzandidzera liti?Ndidzayenda m'nyumba mwanu ndi mtima wangwiro.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 101
Onani Masalmo 101:2 nkhani