15 Ndi vinyo wokondweretsa mtima wa munthu,Ndi mafuta akunyezimiritsa nkhope yace,Ndi mkate wakulimbitsa mtima wa munthu.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 104
Onani Masalmo 104:15 nkhani