Masalmo 106:47 BL92

47 Tipulumutseni, Yehova, Mulungu wathu,Ndi kutisokolotsa kwa amitundu,Kuti tiyamike dzina lanu loyera,Ndi kudzitamandira naco cilemekezo canu.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 106

Onani Masalmo 106:47 nkhani