9 Anatumizira anthu ace cipulumutso;Analamulira cipangano cace kosatha;Dzina lace ndilo loyera ndi loopedwa.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 111
Onani Masalmo 111:9 nkhani