10 Woipa adzaziona, nadzapsa mtima;Adzakukuta mano, nadzasungunuka;Cokhumba oipa cidzatayika.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 112
Onani Masalmo 112:10 nkhani