Masalmo 116:16 BL92

16 Ndiloleni, Yehova, indetu ndine mtumiki wanu;Ndine mtumiki wanu, mwana wa mdzakazi wanu;Mwandimasulira zondimanga,

Werengani mutu wathunthu Masalmo 116

Onani Masalmo 116:16 nkhani