1 Yamikani Yehova; pakuti Iye ndiye wabwino;Pakuti cifundo cace ncosatha.
2 Anene tsono Israyeli,Kuti cifundo cace ncosatha.
3 Anene tsono nyumba ya Aroni,Kuti cifundo cace ncosatha.
4 Anene tsono iwo akuopa Yehova,Kuti cifundo cace ncosatha.
5 M'mene ndinasautsika ndinaitanira pa Yehova;Anandiyankha Dandiika motakasuka Yehova.