159 Penyani kuti ndikonda malangizo anu;Mundipatse moyo, Yehova, monga mwa cifundo canu.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 119
Onani Masalmo 119:159 nkhani