34 Mundizindikiritse, ndipo ndidzasunga malamulo anu;Ndidzawasamalira ndi mtima wanga wonse.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 119
Onani Masalmo 119:34 nkhani