1 Ndikweza maso anga kumapiri:Thandizo langa lidzera kuti?
2 Thandizo langa lidzera kwa Yehova,Wakulenga zakumwamba ndi dziko lapansi.
3 Sadzalola phazi lako literereke:Iye amene akusunga sadzaodzera.
4 Taonani, wakusunga IsrayeaSadzaodzera kapena kugona.