5 Koma iwo akupatuka kutsata njira zao zokhotakhota,Yehova adzawacotsa pamodzi ndi ocita zopanda pace.Mtendere ukhale pa Israyeli.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 125
Onani Masalmo 125:5 nkhani