5 Acite manyazi nabwerere m'mbuyo.Onse akudana naye Ziyoni.
6 Akhale ngati udzu womera patsindwi,Wakufota asanauzule;
7 Umene womweta sadzaza nao dzanja lace,Kapena womanga mitolo sakupatira manja.
8 Angakhale opitirirapo sanena,Dalitso la Mulungu likhale pa inu;Tikudalitsani m'dzina la Yehova.