15 Ndidzadalitsatu cakudya cace;Aumphawi ace ndidzawakhutitsa ndi mkate.
16 Ndipo ansembe ace ndidzawabveka ndi cipulumutso:Ndi okondedwa ace adzapfuulitsa mokondwera.
17 Apo ndidzaphukitsira Davide nyanga;Ndak onzeraru wodzozedwa wanga nyali.
18 Ndidzawabvekaadani ace ndi manyaziKoma pa iyeyu korona wace adzambveka.