4 Mafumu onse a pa dziko lapansi adzakuyamikani,Yehova, popeza adamva mau a pakamwa panu.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 138
Onani Masalmo 138:4 nkhani